-
Machitidwe 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pamene Herode ankakonza zoti abweretse Petulo kwa anthu, usiku umenewo Petuloyo anagona pakati pa asilikali awiri atamumanga ndi maunyolo awiri. Pakhomo panalinso alonda omwe ankalondera ndendeyo.
-