Machitidwe 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mwadzidzidzi, mngelo wa Yehova* anafika,+ ndipo mʼchipinda cha ndendeyo munawala. Kenako mngeloyo anadzutsa Petulo pomugwedeza mʼnthiti nʼkunena kuti: “Dzuka msanga!” Atatero maunyolo amene anamumanga nawo manjawo anagwa pansi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:7 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, tsa. 12
7 Koma mwadzidzidzi, mngelo wa Yehova* anafika,+ ndipo mʼchipinda cha ndendeyo munawala. Kenako mngeloyo anadzutsa Petulo pomugwedeza mʼnthiti nʼkunena kuti: “Dzuka msanga!” Atatero maunyolo amene anamumanga nawo manjawo anagwa pansi.+