-
Machitidwe 12:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Atapitirira gulu loyamba la asilikali apageti ndi lachiwiri, anafika pageti lachitsulo lotulukira popita mumzinda, ndipo linatseguka lokha. Atatuluka anayenda limodzi msewu umodzi, ndipo mwadzidzidzi mngelo uja anachoka.
-