Machitidwe 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ayuda amene anabwera kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala nʼkumukokera kunja kwa mzindawo poganiza kuti wafa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:19 Nsanja ya Olonda,11/1/2015, tsa. 13
19 Ndiyeno Ayuda amene anabwera kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala nʼkumukokera kunja kwa mzindawo poganiza kuti wafa.+