-
Machitidwe 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Atalengeza uthenga wabwino mumzindawu nʼkuphunzitsa anthu ambiri ndithu kuti akhale ophunzira, anabwerera ku Lusitara, ku Ikoniyo ndi ku Antiokeya.
-