Machitidwe 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pochoka kumeneko anayenda ulendo wapamadzi kubwerera ku Antiokeya. Kumeneku nʼkumene mʼmbuyomo abale anawasankha kuti Mulungu awasonyeze kukoma mtima kwakukulu nʼcholinga choti agwire ntchito, yomwe tsopano pa nthawiyi anali ataimaliza.+
26 Pochoka kumeneko anayenda ulendo wapamadzi kubwerera ku Antiokeya. Kumeneku nʼkumene mʼmbuyomo abale anawasankha kuti Mulungu awasonyeze kukoma mtima kwakukulu nʼcholinga choti agwire ntchito, yomwe tsopano pa nthawiyi anali ataimaliza.+