Machitidwe 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Paulo anasonyeza kuti akufuna kumutenga pa ulendo wake. Choncho anamutenga nʼkumudula chifukwa cha Ayuda amene anali kumeneko,+ popeza onse ankadziwa kuti bambo ake ndi Mgiriki. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 122 Nsanja ya Olonda,11/1/2015, tsa. 145/15/2008, tsa. 3212/1/2003, tsa. 206/15/1990, tsa. 1411/15/1989, ptsa. 11-12
3 Paulo anasonyeza kuti akufuna kumutenga pa ulendo wake. Choncho anamutenga nʼkumudula chifukwa cha Ayuda amene anali kumeneko,+ popeza onse ankadziwa kuti bambo ake ndi Mgiriki.
16:3 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 122 Nsanja ya Olonda,11/1/2015, tsa. 145/15/2008, tsa. 3212/1/2003, tsa. 206/15/1990, tsa. 1411/15/1989, ptsa. 11-12