Machitidwe 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼmizinda yonse imene ankadutsa, ankapatsa okhulupirira akumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, mogwirizana ndi zimene atumwi ndiponso akulu ku Yerusalemu anagamula.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 123 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54
4 Mʼmizinda yonse imene ankadutsa, ankapatsa okhulupirira akumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, mogwirizana ndi zimene atumwi ndiponso akulu ku Yerusalemu anagamula.+