-
Machitidwe 16:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho anthu mʼmipingo anapitiriza kukhala ndi chikhulupiriro cholimba ndipo chiwerengero chinkawonjezeka tsiku ndi tsiku.
-