-
Machitidwe 16:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Atangoona masomphenya amenewo, tinaganiza zopita ku Makedoniya. Tinatsimikiza kuti Mulungu watiitana kuti tikalengeze uthenga wabwino kwa anthu akumeneko.
-