-
Machitidwe 16:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho tinanyamuka ulendo wapanyanja kuchokera ku Torowa kupita ku Samatirake. Koma tsiku lotsatira tinafika ku Neapoli.
-