Machitidwe 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Titachoka kumeneko tinafika ku Filipi,+ mzinda wolamulidwa ndi Aroma, umenenso ndi likulu la chigawo cha Makedoniya. Tinakhala mumzindawu kwa masiku angapo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:12 Nsanja ya Olonda,9/15/1996, tsa. 276/15/1990, ptsa. 15-16
12 Titachoka kumeneko tinafika ku Filipi,+ mzinda wolamulidwa ndi Aroma, umenenso ndi likulu la chigawo cha Makedoniya. Tinakhala mumzindawu kwa masiku angapo.