-
Machitidwe 16:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Tsiku la sabata tinatuluka pageti nʼkupita mʼmbali mwa mtsinje, kumene tinkaganiza kuti kuli malo opempherera. Kenako tinakhala pansi nʼkuyamba kulankhula ndi azimayi amene anasonkhana kumeneko.
-