Machitidwe 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno pamene tinkapita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu, chiwanda cholosera zamʼtsogolo.+ Iye ankachititsa kuti mabwana ake azipindula kwambiri chifukwa cha zoloserazo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:16 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, tsa. 76/15/1990, tsa. 16 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 95-96
16 Ndiyeno pamene tinkapita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu, chiwanda cholosera zamʼtsogolo.+ Iye ankachititsa kuti mabwana ake azipindula kwambiri chifukwa cha zoloserazo.