Machitidwe 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma mabwana ake aja ataona kuti sapindulanso,+ anagwira Paulo ndi Sila nʼkuwakokera mumsika, kubwalo la olamulira.+
19 Koma mabwana ake aja ataona kuti sapindulanso,+ anagwira Paulo ndi Sila nʼkuwakokera mumsika, kubwalo la olamulira.+