Machitidwe 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atawakwapula zikoti zambiri, anawatsekera mʼndende ndi kulamula woyangʼanira ndende kuti aziwalondera nʼcholinga choti asathawe.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:23 Nsanja ya Olonda,2/15/1999, ptsa. 27-28
23 Atawakwapula zikoti zambiri, anawatsekera mʼndende ndi kulamula woyangʼanira ndende kuti aziwalondera nʼcholinga choti asathawe.+