Machitidwe 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo Yasoni wawalandira ngati alendo ake. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo a Kaisara. Eti akunena kuti kulinso mfumu ina dzina lake Yesu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:7 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 135-136 Nsanja ya Olonda,6/1/2012, tsa. 20
7 Ndipo Yasoni wawalandira ngati alendo ake. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo a Kaisara. Eti akunena kuti kulinso mfumu ina dzina lake Yesu.”+