Machitidwe 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Ayuda ochokera ku Tesalonika atamva kuti Paulo akufalitsanso mawu a Mulungu ku Bereya, anapitanso kumeneko kukachititsa anthu kuti akwiyire atumwiwo nʼkuyambitsa chipolowe.+
13 Koma Ayuda ochokera ku Tesalonika atamva kuti Paulo akufalitsanso mawu a Mulungu ku Bereya, anapitanso kumeneko kukachititsa anthu kuti akwiyire atumwiwo nʼkuyambitsa chipolowe.+