-
Machitidwe 17:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Mwachitsanzo, pamene ndimadutsa nʼkumayangʼanitsitsa zinthu zimene mumalambira, ndapezanso guwa lansembe lolembedwa kuti, ‘Kwa Mulungu Wosadziwika.’ Choncho ine ndikulalikira kwa inu za Mulungu wosadziwika amene mukumulambirayo.
-