-
Machitidwe 17:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Koma anthu ena anakhala kumbali yake ndipo anakhala otsatira a Yesu. Ena mwa iwo anali Diyonisiyo, woweruza mʼbwalo la Areopagi, mayi wina dzina lake Damarisi komanso anthu ena.
-