Machitidwe 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sila+ ndi Timoteyo+ atafika kuchokera ku Makedoniya, Paulo anatanganidwa kwambiri ndi ntchito yolalikira mawu a Mulungu. Iye ankachitira umboni kwa Ayuda ndiponso kuwatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:5 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151 Utumiki wa Ufumu,4/2001, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,7/1/1991, tsa. 28
5 Sila+ ndi Timoteyo+ atafika kuchokera ku Makedoniya, Paulo anatanganidwa kwambiri ndi ntchito yolalikira mawu a Mulungu. Iye ankachitira umboni kwa Ayuda ndiponso kuwatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+
18:5 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151 Utumiki wa Ufumu,4/2001, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,7/1/1991, tsa. 28