Machitidwe 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, iye anachoka kumeneko* nʼkupita kunyumba ya munthu wina dzina lake Titiyo Yusito. Munthuyu anali wolambira Mulungu ndipo nyumba yake inali moyandikana ndi sunagoge. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:7 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, ptsa. 18-19
7 Zitatero, iye anachoka kumeneko* nʼkupita kunyumba ya munthu wina dzina lake Titiyo Yusito. Munthuyu anali wolambira Mulungu ndipo nyumba yake inali moyandikana ndi sunagoge.