Machitidwe 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mʼmalomwake, anatsanzikana nawo nʼkuwauza kuti: “Yehova* akalola ndidzabweranso kudzakuonani.” Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wapanyanja Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:21 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160
21 Mʼmalomwake, anatsanzikana nawo nʼkuwauza kuti: “Yehova* akalola ndidzabweranso kudzakuonani.” Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wapanyanja