Machitidwe 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo anafika ku Kaisareya. Kenako anapita* kukapereka moni ku mpingo ndipo pambuyo pake anapita ku Antiokeya.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 154
22 ndipo anafika ku Kaisareya. Kenako anapita* kukapereka moni ku mpingo ndipo pambuyo pake anapita ku Antiokeya.+