Machitidwe 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma tinayamba ulendo wapanyanja ku Filipi masiku a Mkate Wopanda Zofufumitsa+ atatha. Ndipo tinawapeza ku Torowa patapita masiku 5. Kumeneko tinakhalako masiku 7. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 168
6 Koma tinayamba ulendo wapanyanja ku Filipi masiku a Mkate Wopanda Zofufumitsa+ atatha. Ndipo tinawapeza ku Torowa patapita masiku 5. Kumeneko tinakhalako masiku 7.