-
Machitidwe 20:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Pa tsiku loyamba la mlungu, titasonkhana pamodzi kuti tidye chakudya, Paulo anayamba kuwakambira nkhani, chifukwa kunali koti anyamuka tsiku lotsatira. Ndipo analankhula kwa nthawi yaitali mpaka pakati pa usiku.
-