-
Machitidwe 20:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Tsopano ife tinatsogola kukakwera ngalawa nʼkuyamba ulendo wopita ku Aso. Iye anatiuza kuti titsogole ndipo tikamutengere ku Aso chifukwa ankafuna kuyenda wapansi.
-