-
Machitidwe 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mʼmawa wake titachoka kumeneko, tinafika pafupi ndi Kiyo. Koma tsiku lotsatira tinaima kwa kanthawi ku Samo, ndipo mʼmawa wake tinafika ku Mileto.
-