Machitidwe 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinkachitira zinthu pa nthawi yomwe ndinali nanu, kuchokera tsiku limene ndinafika mʼchigawo cha Asia.+
18 Akuluwo atafika, iye anawauza kuti: “Inu mukudziwa bwino mmene ndinkachitira zinthu pa nthawi yomwe ndinali nanu, kuchokera tsiku limene ndinafika mʼchigawo cha Asia.+