Machitidwe 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho khalani maso, ndipo muzikumbukira kuti kwa zaka zitatu+ masana ndi usiku, sindinasiye kuchenjeza aliyense wa inu ndikutulutsa misozi. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:31 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 33
31 Choncho khalani maso, ndipo muzikumbukira kuti kwa zaka zitatu+ masana ndi usiku, sindinasiye kuchenjeza aliyense wa inu ndikutulutsa misozi.