Machitidwe 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anafika kwa ife nʼkutenga lamba wa Paulo. Kenako anadzimanga mapazi ndi manja nʼkunena kuti: “Mzimu woyera wati, ‘Mwiniwake wa lambayu, Ayuda adzamumanga chonchi ku Yerusalemu+ nʼkumupereka kwa anthu a mitundu ina.’”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:11 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 177-178, 189 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, ptsa. 22-23
11 Iye anafika kwa ife nʼkutenga lamba wa Paulo. Kenako anadzimanga mapazi ndi manja nʼkunena kuti: “Mzimu woyera wati, ‘Mwiniwake wa lambayu, Ayuda adzamumanga chonchi ku Yerusalemu+ nʼkumupereka kwa anthu a mitundu ina.’”+