-
Machitidwe 21:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Paulo anawapatsa moni nʼkuyamba kuwafotokozera mwatsatanetsatane zimene Mulungu anachitira anthu a mitundu ina kudzera mu utumiki wake.
-