-
Machitidwe 21:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Choncho mumzinda wonsewo munali chisokonezo ndipo anthu anathamangira kukachisiko. Kenako anagwira Paulo nʼkumukokera kunja kwa kachisi. Nthawi yomweyo zitseko zinatsekedwa.
-