-
Machitidwe 21:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Nthawi yomweyo, iye anatenga asilikali ndi atsogoleri awo nʼkuthamangira kumeneko. Anthuwo ataona mkulu wa asilikali uja pamodzi ndi asilikali akewo, anasiya kumenya Paulo.
-