Machitidwe 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zitatero mkulu wa asilikaliyo anafika pafupi nʼkumugwira ndipo analamula kuti amumange ndi maunyolo awiri.+ Kenako anafunsa anthu zokhudza iyeyo komanso zimene wachita. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:33 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, tsa. 216/15/1990, ptsa. 22-23
33 Zitatero mkulu wa asilikaliyo anafika pafupi nʼkumugwira ndipo analamula kuti amumange ndi maunyolo awiri.+ Kenako anafunsa anthu zokhudza iyeyo komanso zimene wachita.