-
Machitidwe 21:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Koma ena pagululo anayamba kufuula zinthu zina, ena zina. Choncho atalephera kutolapo mfundo yeniyeni chifukwa cha phokoso, analamula kuti apite naye kumpanda wa asilikali.
-