-
Machitidwe 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipotu mkulu wa ansembe ndi bungwe lonse la akulu angandichitire umboni. Kwa amenewa nʼkumene ndinapezanso makalata ondiloleza kuti ndikamange abale ku Damasiko. Ndinanyamuka kuti ndikagwire anthu omwe anali kumeneko nʼkuwabweretsa ku Yerusalemu atamangidwa kuti adzapatsidwe chilango.
-