Machitidwe 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndili mʼnjira, nditatsala pangʼono kufika ku Damasiko, dzuwa lili pamutu, mwadzidzidzi kunawala kwambiri. Kuwala kumeneku kunali kochokera kumwamba ndipo kunazungulira pamene ine ndinali.+
6 Koma ndili mʼnjira, nditatsala pangʼono kufika ku Damasiko, dzuwa lili pamutu, mwadzidzidzi kunawala kwambiri. Kuwala kumeneku kunali kochokera kumwamba ndipo kunazungulira pamene ine ndinali.+