-
Machitidwe 22:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ine ndinayankha kuti, ‘Ndinu ndani Mbuyanga?’ Ndipo anandiuza kuti, ‘Ndine Yesu wa ku Nazareti, amene iwe ukumuzunza.’
-