Machitidwe 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiye ine ndinati, ‘Nditani Ambuye?’ Ambuyewo anandiuza kuti, ‘Nyamuka ndipo upite ku Damasiko. Kumeneko ukauzidwa zonse zimene zakonzedwa kuti uchite.’+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:10 Nsanja ya Olonda,10/15/2012, ptsa. 28-29
10 Ndiye ine ndinati, ‘Nditani Ambuye?’ Ambuyewo anandiuza kuti, ‘Nyamuka ndipo upite ku Damasiko. Kumeneko ukauzidwa zonse zimene zakonzedwa kuti uchite.’+