-
Machitidwe 22:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma popeza sindinkatha kuona chilichonse chifukwa cha ulemerero wa kuwalako, anthu amene ndinali nawo aja, anandigwira dzanja mpaka kukafika ku Damasiko.
-