Machitidwe 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiye ukuchedweranji? Nyamuka ubatizidwe nʼkuchotsa machimo ako+ poitanira pa dzina lake.’+