Machitidwe 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma nditabwerera ku Yerusalemu+ nʼkuyamba kupemphera mʼkachisi, ndinaona masomphenya.