Machitidwe 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼmasomphenyawo ndinaona Ambuye akundiuza kuti, ‘Tuluka mu Yerusalemu mwamsanga, chifukwa iwo sadzamva uthenga wako wonena za ine.’+
18 Mʼmasomphenyawo ndinaona Ambuye akundiuza kuti, ‘Tuluka mu Yerusalemu mwamsanga, chifukwa iwo sadzamva uthenga wako wonena za ine.’+