Machitidwe 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ine ndinanena kuti, ‘Ambuye, iwowo akudziwa bwino kuti ndinkapita mʼmasunagoge nʼkumatsekera mʼndende ndiponso kukwapula anthu amene ankakukhulupirirani.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:19 Nsanja ya Olonda,6/15/2007, tsa. 17
19 Ndipo ine ndinanena kuti, ‘Ambuye, iwowo akudziwa bwino kuti ndinkapita mʼmasunagoge nʼkumatsekera mʼndende ndiponso kukwapula anthu amene ankakukhulupirirani.+