-
Machitidwe 22:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Iwo ankamumvetsera mpaka pa mawu amenewa. Koma kenako anafuula kuti: “Munthu ameneyu asapezekenso padziko lapansi! Sakuyenera kukhala ndi moyo!”
-