Machitidwe 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma atamugoneka kuti amukwapule, Paulo anafunsa mtsogoleri wa asilikali amene anaima pamenepo kuti: “Kodi malamulo amakulolani kukwapula nzika ya Roma mlandu wake usanazengedwe?”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:25 Nsanja ya Olonda,3/1/2015, tsa. 1212/15/2001, tsa. 22
25 Koma atamugoneka kuti amukwapule, Paulo anafunsa mtsogoleri wa asilikali amene anaima pamenepo kuti: “Kodi malamulo amakulolani kukwapula nzika ya Roma mlandu wake usanazengedwe?”+