-
Machitidwe 22:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Mtsogoleri wa asilikaliyo atamva zimenezi, anapita kwa mkulu wa asilikali nʼkukamuuza kuti: “Mukufuna kuchita chiyani? Munthuyutu ndi nzika ya Roma.”
-