Machitidwe 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo amuna amene ankafuna kumufunsa mafunso, uku akumukwapula, anachoka nʼkumusiya. Nayenso mkulu wa asilikali uja anachita mantha atadziwa kuti munthu amene anamumangayo ndi nzika ya Roma.+
29 Nthawi yomweyo amuna amene ankafuna kumufunsa mafunso, uku akumukwapula, anachoka nʼkumusiya. Nayenso mkulu wa asilikali uja anachita mantha atadziwa kuti munthu amene anamumangayo ndi nzika ya Roma.+