Machitidwe 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsiku lotsatira, pofuna kudziwa chenicheni chimene Ayudawo ankamuimbira mlandu, anamutulutsa. Atatero analamula ansembe aakulu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda kuti asonkhane. Ndiyeno anabweretsa Paulo nʼkumuimika pakati pawo.+
30 Tsiku lotsatira, pofuna kudziwa chenicheni chimene Ayudawo ankamuimbira mlandu, anamutulutsa. Atatero analamula ansembe aakulu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda kuti asonkhane. Ndiyeno anabweretsa Paulo nʼkumuimika pakati pawo.+